Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa
  • Mzinda wa Rostock, m’dziko la Germany​—Akulalikira padoko ndipo akuwerengera anthu lemba la m’Baibulo

  • Tawuni ya Marburg, m’dziko la Germany​—Akukambirana za uthenga wa m’Baibulo wonena za m’tsogolo, pafupi ndi msasa wa anthu othawa kwawo

  • Frankfurt, Germany—Akufotokoza mfundo zothandiza zopezeka m’Baibulo

NTCHITO YOLALIKIRA

Amadutsa Pamchenga wa Pansi pa Nyanja Kupita Kokalalikira

A Mboni za Yehova anapeza njira yowathandiza kuti azikalalikira anthu a patizilumba ta Halligen.

MOYO WA PA BETELI

Tsiku Lapadera Lokaona Malo ku Steinfels

Ofesi ya Mboni za Yehova ya ku Central Europe inaitana anthu okhala pafupi, abizinezi ndiponso akukuakulu a boma kuti adzaone maofesiwa. Tsiku lapaderali linali ndi mutu wakuti: “Takwanitsa Zaka 30 Tili ku Selters Kuno.” Kodi ena mwa anthu 3,000 omwe anapita kumalowa ananena zotani?