• Gurgeniani, ku Georgia​—Akugawira kabuku kakuti Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017

Georgia

Werengani nkhani yosangalatsayi ndiponso yolimbikitsa yonena za abale a m’dziko la Georgia.

NSANJA YA OLONDA

Chuma Chomwe Chinabisika kwa Zaka Zambiri

Werengani kuti mudziwe zimene zinachitika kuti akatswiri apeze Baibulo lakale kwambiri la Chijojiya.