• Gjirokastër, Albania​—Akupatsa munthu wina kabuku ka m’Chingelezi kakuti Was Life Created?

Mfundo Zachidule—Albania

  • 2,881,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,642—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 87—Mipingo
  • Pa anthu 514 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi