• Samcheong-dong ku Seoul, South Korea—Akulalikira pogwiritsa ntchito Baibulo

  • Mudzi wa Daraengi, pachilumba cha Namhae-do, m’dziko la South Korea​—Akugawira kabuku kakuti Mverani Mulungu

  • Nonsan-si, Chungnam, South Korea​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo kwa munthu yemwe akutenga zakudya m’mitsuko imene amasungiramo

  • Seoul, South Korea​—Kulalikira m’malo opezeka anthu ambiri