• Tokyo, Japan​—Akugwiritsa ntchito webusaiti ya jw.org kuuza munthu wovutika kumva uthenga wa m’Baibulo

  • Kamaishi, Japan —A Mboni za Yehova akuphunzira ndi anthu amene anapulumuka pa chivomezi ndi tsunami zomwe zinachitika m’chaka cha 2011

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anthu a ku Japan Analandira Mphatso

Kabaibulo katsopano kakuti ‘Uthenga Wabwino Wolembedwa ndi Mateyu’ kanatulitsidwa ku Japan. Kodi kanalembedwa bwanji? N’chifukwa chiyani kanalembedwa?

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Uthenga Wabwino Unayamba Kuwala ku Japan

Makalavani otchedwa Yehu ankathandiza kwambiri polalikira uthenga wa Ufumu ku Japan.

NTCHITO YOFALITSA MABUKU

Ofesi ya Mboni za Yehova ku Japan Ikusindikiza Mabaibulo a Zikuto Zolimba Omwe Akutumizidwa M’madera Osiyanasiyana Padziko Lapansili

A Mboni za Yehova aika makina okonzera mabuku kufakitale yawo ya ku Japan. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri zokhudza makina amenewa.