• Istanbul, Turkey​—Akugawira magazini a Galamukani! a m’Chitekishi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Turkey

Mu 2014, kunali ntchito yapadera yolalikira ku Turkey. N’chifukwa chiyani ntchito yapaderayi inachitika? Kodi zotsatirapo zake zinali zotani?