• Barcelona, Spain—A Mboni m’derali amalalikira m’zinenero monga Chiarabu, Chikatalani, Chingelezi, Chifulenchi, Chisipanishi komanso Chiudu

  • Ku Agaete pa zilumba za Canary m’dziko la Spain—Akugawira kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu!

ZOCHITIKA PA MOYO

Nyumba Imene Munayesedwera Chikhulupiriro cha a Mboni Ena

Nyumba ya ku Spain yomwe inali ndende ya a Mboni za Yehova ambirimbiri omwe anakana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira.

GALAMUKANI!

Dziko la Spain

Ku Spain kuli mitundu yambiri ya anthu komanso zinthu zachilengedwe zosiyanasiyana zochititsa chidwi. Ku Spain n’kumene kumapezeka mafuta a maolivi ambiri kuposa mayiko ena onse padziko lapansi.

NTCHITO YOFALITSA MABUKU

Gulu la Anthu Omasulira Chisipanishi Lasamukira ku Spain

Kuyambira mu 1907, mabuku othandiza anthu kumvetsa Baibulo ofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova anayamba kumasuliridwa m’Chisipanishi. Werengani zokhudza ntchito yomasulira mabuku awo m’Chisipanishi.