Mfundo Zachidule—Cape Verde
- 514,000—Chiwerengero cha anthu
- 2,277—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 35—Mipingo
- Pa anthu 228 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi


Mzinda wa Mindelo, m’dziko la Cape Verde—Akugawira kabuku kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu