• Gombe la Anse Vata ku Nouméa, New Caledonia—Akukambirana ndi munthu pogwiritsa ntchito Baibulo

Mfundo Zachidule—New Caledonia

  • 284,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,489—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 32—Mipingo
  • Pa anthu 114 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi