Mfundo Zachidule—Timor-Leste
- 1,415,000—Chiwerengero cha anthu
- 449—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 6—Mipingo
- Pa anthu 3,546 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
MBIRI YA MOYO WANGA
Warren Reynolds: Ndimasangalala Kuti Ndinasankha Zoyenera
A Warren ndi akazi awo a Leann, aona mmene Yehova amathandizira anthu kukhala chilichonse chimene iye akufuna, bola ngati anthuwo ali ofunitsitsa ndi mtima wonse kuchita utumikiwo.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
“Panopa Ndimakonda Kwambiri Utumiki”
Mbiri ya moyo wanga: Vanessa Vicini

