• Msewu wa San José ku San Juan, Puerto Rico—Akugawira buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

  • San Juan, Puerto Rico—Akuyankha funso la m’Baibulo pafupi ndi El Morro yomwe ndi nyumba yakale imene asilikali ankabisalamo ndipo yakhala zaka pafupifupi 500

Mfundo Zachidule—Puerto Rico

  • 3,659,000—Chiwerengero cha anthu
  • 23,632—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 299—Mipingo
  • Pa anthu 155 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi