• Guna Yala, Panama​—Akulalikira kwa msodzi wachiguna pachilumba cha Nurdub (Aguna poyamba ankatchedwa Akuna)

GALAMUKANI!

Panama

Ku Panama n’kotchuka kwambiri chifukwa cha ngalande zake. Werengani kuti mumve zambiri za anthu amene amkhala m’dziko limeneli.