Mboni za Yehova Padziko Lonse

Curacao

  • Ku Punda, mu mzinda wa Willemstad m’dziko la Curaçao. Akuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

  • Ku Punda, mu mzinda wa Willemstad m’dziko la Curaçao. Akuwerenga vesi la m’Baibulo lomwe lili m’kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale

  • Ku Punda, mumzinda wa Willemstad m’dziko la Curaçao. Akulalikira uthenga wa m’Baibulo khomo ndi khomo