• Zarcero, Costa Rica​—Kukambirana mfundo za m’Baibulo ndi woweta ng’ombe m’dera la kunja kwa mzinda

GALAMUKANI!

Dziko la Costa Rica

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake anthu a m’dzikoli amadziwika kuti Atiko.