• Palacio de Bellas Artes, Mexico City, Mexico—Akuphunzitsa pogwiritsa ntchito Baibulo

  • Tauni ya Betania, m’dera la Chiapas, m’dziko la Mexico​—Akugawira kabuku kofotokoza Baibulo m’chilankhulo cha Chitsotsilu

  • Mzinda wa San Miguel de Allende, m’dera la Guanajuato, m’dziko la Mexico​—Akuwerengera munthu lemba lolimbikitsa la m’Baibulo

NTCHITO ZOMANGAMANGA

A Mboni za Yehova Akumanga Nyumba za Ufumu Zambiri

Kuyambira mu 1999, a Mboni za Yehova amanga Nyumba za Ufumu zoposa 5,000 ku Mexico ndiponso mayiko ena 7 a ku Central America. N’chifukwa chiyani anthu ena omwe si a Mboni amafunitsitsa Nyumba za Ufumu zitamangidwa m’dera lawo?

KUTHANDIZA ENA

Ntchito Imene Inathandiza Anthu Kuti Asadziphe

N’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova anakonza zoti kwa miyezi iwiri agwire ntchito yapadera yolalikira m’dera la Tabasco ku Mexico? Kodi ntchitoyi inathandiza bwanji anthu?

MOYO WA PA BETELI

Anthu Ambiri Anakaona Ofesi ya Nthambi ya Central America

Kwa anthu ena, sizinali zophweka kuti apite kukaona ofesi ya nthambi. Ambiri anayenda kwa masiku angapo pa mabasi omwe anapanga hayala. Kodi ana komanso achinyamata ananena chiyani atapita kukaona Beteli?

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Mexico

Werengani kuti mumve kuti ndi achinyamata angati amene apirira mavuto osiyanasiyana ndi cholinga choti awonjezere zimene amachita mu utumiki.

MOYO WA PA BETELI

Ophunzira a pa Yunivesite Ina Anakaona Ofesi ya Nthambi ya Mboni za Yehova ku Mexico

Ophunzira a pa yunivesite yotchedwa National School of Library and Archival Sciences anakaona ofesi yathu ku Mexico. Wophunzira m’modzi anaona kuti ulendowu unamuthandiza kusiya tsankho.

KUTHANDIZA ENA

A Mboni za Yehova Analandira Satifiketi Yaulemu Chifukwa Choteteza Chilengedwe

Fakitale ya Mboni za Yehova yosindikiza mabuku ku Mexico yakhala ikulandira satifiketi yaulemu kwa zaka 7 zotsatizana chifukwa choteteza chilengedwe.