• Pafupi ndi Calbuco volcano, Chile​—Akukambirana zimene Baibulo limatilonjeza zoti anthu adzakhala ndi moyo wosatha padziko lapansi

  • Valparaiso, Chile​—Akuwerenga lemba m’Baibulo

  • Pafupi ndi Calbuco volcano, Chile​—Akukambirana zimene Baibulo limatilonjeza zoti anthu adzakhala ndi moyo wosatha padziko lapansi

  • Valparaiso, Chile​—Akuwerenga lemba m’Baibulo

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anabala Zipatso Chifukwa Chokonzekera Bwino

Werengani kuti mudziwe mmene mtsikana wina wazaka 10 ku Chile anagwirira ntchito mwakhama kuti aitanire aliyense ku sukulu kwake amene amalankhula chinenero cha Chimapudunguni ku mwambo wofunika kwambiri.