Chile
A Mboni Anathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Madzi Osefukira ku Chile
Madzi atangosefukira ku Chile a Mboni anayamba kuthandiza anthu.
Moto Wolusa Wawononga Zinthu ku Valparaíso, Chile
Moto wolusa wawononga zinthu mumzinda wa Valparaíso. Ngoziyi itangochitika, a Mboni za Yehova anakhazikitsa makomiti othandiza anthu omwe akhudzidwa ndi ngoziyi.