Mfundo Zachidule—French Guiana
- 292,000—Chiwerengero cha anthu
- 3,045—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 43—Mipingo
- Pa anthu 98 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
ZOCHITIKA PA MOYO
Ulendo Wokalalikira kwa Anthu Okhala M’mphepete mwa Mtsinje wa Maroni
A Mboni za Yehova 13 akunyamuka pa ulendo wokalalikira uthenga wa m’Baibulo wopatsa chiyembekezo kwa anthu okhala m’madera akutali m’nkhalango ya Amazon ku South America.

