Pitani ku nkhani yake

  • Paris, France​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo pafupi ndi mtsinje wa Seine

KUTHANDIZA ENA

A Mboni za Yehova Analimbikitsa Anthu ku France

A Mboni za Yehova anaika timashelefu ta mabuku m’malo osiyanasiyana ku mpikisano wa njinga wa ku France pofuna kuuza anthu uthenga wolimbikitsa komanso wotonthoza.

NTCHITO YOLALIKIRA

Kulalikira Mumzinda wa Paris

A Mboni za Yehova anagwira ntchito yodziwitsa anthu za nthawi imene anthu sadzawononganso chilengedwe padzikoli.

NTCHITO YOLALIKIRA

Ku France Kunachitika Chionetsero Chapadera cha Baibulo

Anthu amene anapita kuchionetsero cha zinthu za m’mayiko osiyanasiyana cha 2014 chomwe chinali mumzinda wa Rouen ku France anachita chidwi kwambiri ndi malo ena omwe analembapo kuti ‘Baibulo ndi Lothandiza Kuyambira Kale, Panopa Komanso M’tsogolo.’

NTCHITO YOLALIKIRA

Anthu Okonda Mtendere Anasonkhana pa Mwambo wa Armada

A Mboni za Yehova anagwiritsa ntchito matebulo a matayala popereka mabuku kwa ulele kwa anthu amene anabwera ku mwambo umene unachitikira ku France.