• Jabbeke, Belgium​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo pamalo oimika galimoto, mumsewu wa E40 Trans-European Motorway

Mfundo Zachidule—Belgium

  • 11,431,000—Chiwerengero cha anthu
  • 25,173—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 336—Mipingo
  • Pa anthu 459 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi