Mboni za Yehova Padziko Lonse

Ecuador

  • Chambo, Ecuador—Akugawa kabuku mu chinenero cha Quichua

Mfundo Zachidule—Ecuador

  • 18,104,000—Chiwerengero cha anthu
  • 104,393—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,190—Mipingo
  • Pa anthu 176 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Anateteza Ufulu wa Kulambira wa Anthu Akumidzi

Pamene anthu otsutsa anaphwanyira a Mboni za Yehova ufulu wawo wa kulambira, abale athu anawathandiza mwamsanga.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Ecuador