Mboni za Yehova Padziko Lonse

Palestinian Territory

Mfundo Zachidule—Palestinian Territory

  • 5,745,000—Chiwerengero cha anthu
  • 81—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 2—Mipingo
  • Pa anthu 71,813 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Kodi Chikondi Komanso Kukhulupirika Zidzagonjetsa Liti Chidani?

N’zovuta kusiya mtima wodana ndi anthu a mtundu wina. Koma taonani zimene Myuda wina komanso munthu wina wa ku Palesitina anachita.

NKHANI

A Mboni za Yehova Akuvutika Kuti Apatsidwe Ufulu Wonse Kudera la Mapalestina

Si bwino kuti a Mboni azichitiridwa tsankho posaloledwa kulembetsa chipembedzo chawo m’kaundula zomwe zikuchititsa kuti asamalandire ufulu wawo wonse.