Mfundo Zachidule—Myanmar
- 51,317,000—Chiwerengero cha anthu
- 5,382—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 115—Mipingo
- Pa anthu 9,677 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Myanmar
Kodi n’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova ambiri achoka kwawo kuti akathandize pa ntchito yolalikira ku Myanmar?

