Pitani ku nkhani yake

  • Zagreb, Croatia​—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda mumsewu wotchedwa Ilica Street

  • Ku Rovinj m’dziko la Croatia​—Akuphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

  • Mu mzinda wa Zagreb ku Croatia—Akugawira kapepala ka Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?

  • Mu mzinda wa Zagreb ku Croatia—Akulalikira uthenga wopatsa chiyembekezo umene umapezeka m’Baibulo

  • Pula, Croatia​—Akugawira kapepala kakuti Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo? pafupi ndi bwalo lamasewero la ku Rome.

  • Rovinj, Croatia​—Akulalikira zokhudza Ufumu wa Mulungu.

Mfundo Zachidule—Croatia

  • 4,284,889—Chiwerengero cha anthu
  • 5,206—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 60—Mipingo
  • Pa anthu 823 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi