• Kupul, Guinea-Bissau—Akukambirana mfundo za m’Baibulo ndi mlimi m’chinenero cha Chipwitikizi cha Chikiliyo

Mfundo Zachidule—Guinea-Bissau

  • 1,921,000—Chiwerengero cha anthu
  • 191—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 3—Mipingo
  • Pa anthu 10,440 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi