Mfundo Zachidule—Andorra
- 88,000—Chiwerengero cha anthu
- 177—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 3—Mipingo
- Pa anthu 524 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi


Mzinda wa Andorra la Vella m’dziko la Andorra—Akuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? m’chilankhulo cha Chikatalani