• N’Djamena, Chad —Akulalikira zokhudza Ufumu wa Mulungu

Mfundo Zachidule—Chad

  • 15,000,000—Chiwerengero cha anthu
  • 847—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 19—Mipingo
  • Pa anthu 17,710 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi