• Dera la Štrbské Pleso ku Slovakia—Akugawira kapepala kakuti Kodi Dziko Lapansili Lili M’manja mwa Ndani?

Mfundo Zachidule—Slovakia

  • 5,445,087—Chiwerengero cha anthu
  • 11,293—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 134—Mipingo
  • Pa anthu 482 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi