Mfundo Zachidule—South Africa
- 63,101,000—Chiwerengero cha anthu
- 107,746—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 1,925—Mipingo
- Pa anthu 600 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Ndakhala Ndikusangalala Kutumikira Yehova
Mbiri ya Moyo Wanga: John Kikot
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti
Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?

