• Macao​—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda pafupi ndi mabwinja a tchalitchi cha St. Paul

Mfundo Zachidule—Macao

  • 658,900—Chiwerengero cha anthu
  • 346—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 5—Mipingo
  • Pa anthu 1,904 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi