Mfundo Zachidule—Bosnia and Herzegovina
- 3,140,000—Chiwerengero cha anthu
- 951—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 15—Mipingo
- Pa anthu 3,420 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
A Mboni Anathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Kusefukira kwa Madzi ku Balkans
Nthawi yomweyo a Mboni za Yehova anayamba kuthandiza ndiponso kulimbikitsa anthu omwe anakhudzidwa ndi ngozi ya madzi osefukira ya pa May 2014 yomwe sinachitikepo ku Bosnia-Herzegovina, Croatia ndi Serbia.

