• Mzinda wa Venice, m’dziko la Italy​—Akulalikira pogwiritsa ntchito Baibulo

KUTHANDIZA ENA

A Mboni ku Italy Anathandiza Anthu a M’dera Lawo

Kodi anthu ankafunikira kuthandizidwa motani? A Mboni anathandiza bwanji?

ZOCHITIKA ZAPADERA

Anthu Anasangalala Kwambiri Pamsonkhano wa M’chilankhulo cha Chitagalogi ku Rome

Ku Europe kuli a Mboni za Yehova ambiri amene amalankhula Chitagalogi ndipo msonkhano wa masiku atatuwu unali woyamba kuchitika m’chilankhulo chawo.

GALAMUKANI!

Dziko la Italy

Dziko la Italy limadziwika ndi zinthu zakale, madera osiyanasiyana komanso kuli anthu okonda kucheza. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri za dzikoli komanso zokhudza Mboni za Yehova za kumeneko.

KUTHANDIZA ENA

“Ndinu Anthu Achitsanzo Chabwino Kwambiri”

Madzi osefukira pamodzi ndi matope atawononga mzinda wa Saponara ku Italy, gulu la anthu ongodzipereka linagwira ntchito mwakhama yokonza zinthu zimene zinawonongeka.