Mfundo Zachidule—Thailand
- 70,366,000—Chiwerengero cha anthu
- 5,710—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 148—Mipingo
- Pa anthu 12,552 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
Ofesi ya Kazembe wa ku Thailand “Inayamikira Komanso Kupereka Ulemu” kwa a Mboni za Yehova ku Peru Chifukwa Chothandiza Akaidi a ku Thailand
Oimira Ofesi ya Kazembe wa dziko la Thailand anakayendera a Mboni za Yehova ku Peru kuti akawayamikire chifukwa cha ntchito yawo komanso zimene anachitira akaidi a ku Thailand.
NKHANI
Akuluakulu a Boma la Thailand Akugwiritsa Ntchito Mabuku a Mboni za Yehova Pothandiza Anthu a M’dziko Lawo
Kwa zaka zitatu zapitazi, akuluakulu a boma ku Thailand akhala akugwiritsa ntchito mabuku a Mboni pophunzitsa anthu makhalidwe abwino.

