NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Brazil

NTCHITO ZOMANGAMANGA

M’nkhalango ya Amazon Munamangidwa Nyumba Yochitira Misonkhano

A Mboni ena amayenda paboti kwa masiku atatu kuti akachite msonkhano ku Nyumba Yochitira Misonkhanoyi.

NTCHITO YOLALIKIRA

Kulalikira M’mbali mwa Mtsinje wa Xingu

Gulu la a Mboni za Yehova okwana 28, linagwiritsa ntchito boti lotalika mamita 15 n’cholinga chokalalikira za Ufumu wa Mulungu, kwa anthu a m’midzi ya m’mbali mwa mtsinje wa Xingu.

GALAMUKANI!

Dziko la Brazil

Dziko la Brazil ndi lalikulu pafupifupi hafu ya South America. Werengani kuti mudziwe kumene chikhalidwe cha m’dziko la Brazil chinachokera.