Mfundo Zachidule—Malta
- 545,000—Chiwerengero cha anthu
- 883—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 10—Mipingo
- Pa anthu 629 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi


Birgu, Malta—Akugawira kapepala kakuti, Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?