Kodi mungatani kuti banja lanu lizisangalala?

Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Lizisangalala?

Chichewa
Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Lizisangalala?
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102024303/afrn/art/1102024303_afrn_sqr_xl.jpg
T-fam tsamba 1-2

Kodi mungatani kuti banja lanu lizisangalala?

Kodi mungatani kuti banja lanu lizisangalala?

“Aliyense wa inu azikonda mkazi wake ngati mmene amadzikondera yekha komanso mkazi azilemekeza kwambiri mwamuna wake.”Aefeso 5:33.

Baibulo limanena kuti

  • Anthu okwatirana azikhala okhulupirika m’banja.Mateyu 19:​4-6.

  • Ana amene amalemekeza komanso kumvera makolo awo, zinthu zimawayendera bwino.Aefeso 6:​1-3.

Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.