Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Baibulo Limanena Zoona?
Baibulo limanena kuti malemba onse ndi ochokera kwa Mulungu ndipo iye “sanganame.” (1 Atesalonika 2:13; Tito 1:2) Kodi zimenezi ndi zoona kapena Baibulo ndi buku la nthano chabe?
Nkhani Zina
Mavidiyo Othandiza Kumvetsa Mfundo Zofunika za M’baibulo Mbiri ya Baibulo Mbiri ya Baibulo Baibulo Komanso Sayansi Umboni Wasayansi Wosonyeza Kuti Baibulo Ndi LolondolaMwina Mungakondenso Kudziwa Izi
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Baibulo N’chiyani?
Yambani kufufuza za uthenga wochititsa chidwi wotchedwa mawu a Mulungu.
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Nkhani za M’Baibulo Zimatsutsana?
Onani nkhani zina za m’Baibulo zimene zimaoneka ngati zimatsutsana komanso mfundo zimene zingakuthandizeni kuti mumvetse nkhanizo.
GALAMUKANI!
Baibulo Limanena Zinthu Molondola
Baibulo linafotokoza kalekale zinthu zosiyanasiyana za m’chilengedwe asayansi asanazitulukire n’komwe. Linaneneratunso za kukhalapo ndi kugwa kwa maulamuliro akuluakulu padziko lonse ndiponso lili ndi mayankho ogwira mtima a mafunso ofunika kwambiri.
MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI
Kodi Baibulo la Dziko Latsopano Linamasuliridwa Molondola?
N’chifukwa chiyani Baibulo la Dziko Latsopano limasiyana ndi Mabaibulo ena?
MFUNDO ZOFUNIKA ZA M'BAIBULO
Kodi Analemba Baibulo Ndi Ndani?
Ngati Baibulo linalembedwa ndi anthu, kodi n’zomveka kunena kuti ndi Mawu a Mulungu? Kodi m’Baibulo muli mawu a ndani?
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Yambani Kuphunzira Baibulo
Phunzirani Baibulo kwaulere, mochita kukambirana ndi mphunzitsi wanu.
MFUNDO ZOFUNIKA ZA M'BAIBULO