Pitani ku nkhani yake

Wosaona Ndiponso Wosamva

Wosaona Ndiponso Wosamva

James Ryan, yemwe ndi wa Mboni za Yehova, anabadwa ndi vuto losamva ndipo kenako anakhalanso ndi vuto losaona. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe chifukwa chimene amaonera kuti anthu a m’banja lake ndi a mumpingo, * akumuthandiza kuti asamadzione ngati wopanda pake.

^ ndime 2 Pa anthu onse a m’banja la James, wa Mboni ndi yekha.