ZOTI MUCHITE Mmene Mungasankhire Munthu Womutsanzira YAMBANI Gawoli likuthandizani kusankha munthu wabwino woti muzimutsanzira. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndingasankhe Bwanji Munthu Wabwino Woti Ndizimutsanzira? Kukhala ndi munthu woti muzimutsanzira kungakuthandizeni kupewa mavuto, kukwaniritsa zolinga zanu komanso kuti zinthu zizikuyenderani bwino. Kodi inuyo muyenera kutsanzira munthu wotani? ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndiwonjezere Anzanga? Zimakhala bwino kukhala ndi kagulu kochepa ka anzanu, koma sikuti zimenezi zimathandiza nthawi zonse. N’chifukwa chiyani? ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA N’chifukwa Chiyani Sindikuyenera Kutsanzira Khalidwe la Anthu Omwe Amaonetsedwa M’mafilimu, pa TV ndi M’magazini?—Gawo 1: Ya Atsikana Achinyamata ambiri amaganiza kuti akuchita zinthu m’njira yawoyawo, koma amakhala akungotsanzira zochita za ena. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA N’chifukwa Chiyani Sindikuyenera Kutsanzira Khalidwe la Anthu Omwe Amaonetsedwa M’mafilimu, pa TV ndi M’magazini?—Gawo 2: Ya Anyamata Kodi kutsanzira makhalidwe a anthu amene amasonyezedwa m’mafilimu, pa TV ndi m’magazini kungapangitse kuti anthu asamakopeke nanu? ZIMENE ACHINYAMATA ANZANU AMANENA Cameron Anapeza Moyo Wabwino Kwambiri Kodi mukufuna kukhala munthu wosangalala? Mvetserani pamene Cameron akufotokoza zimene zinamuthandiza kuti akhale wosangalala atapita kumalo amene samaganizira kuti angafikeko. Patsani ena Patsani ena Mmene Mungasankhire Munthu Womutsanzira ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Mmene Mungasankhire Munthu Womutsanzira Chichewa Mmene Mungasankhire Munthu Womutsanzira https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502017187/univ/art/502017187_univ_sqr_xl.jpg