Pitani ku nkhani yake

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Tsanzirani Msamariya Wachifundo

Werengani fanizo la Yesu la Msamariya wachifundo. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.