Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ACHINYAMATA ACHITE

ZOTI MUCHITE

Magemu Amene Ndimasewera pa Zipangizo Zamakono

Tsamba limene lingakuthandizeni kudziwa zochita posankha magemu ndiponso nthawi imene mungamasewere.

Zimene Mungachite Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama

Gwiritsani ntchito zoti muchitezi kuti muone kuchuluka kwa zinthu zofunika ndi zongowonjezera komanso onani ngati zonse zikugwirizana ndi bajeti yanu.

Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu

Onani zimene zingakuthandizeni kukhala osamala musanatumize zithunzi.

Kodi Nthawi Zina Mumasowa Mpata Wochitira Zinthu Panokha?

Onani zimene mungachite kuti makolo anu azikudalirani.