Chichewa
Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502100009/univ/art/502100009_univ_sqr_xl.jpg

MAVIDIYO AMAKATUNI

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Masiku ano kuli nkhani zambirimbiri, kodi mungadziwe bwanji nkhani zoyenera kukhulupirira? Taonani mfundo zimene zingakuthandizeni kudziwa nkhani zoona.