Moyo Wanga Wachinyamata—Kodi N’zomveka Kukhulupirira Kuti Mulungu Alipo? YAMBANI Moyo Wanga Wachinyamata—Kodi N’zomveka Kukhulupirira Kuti Mulungu Alipo? Crystal ndi Elibaldo anafufuza kuti apeze mayankho a mafunso awo. Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Nkhani Zina Zimene Achinyamata Anzanu Amanena Moyo Wauzimu Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi BAIBULO KOMANSO SAYANSI Zokhudza Mmene Moyo Unayambira Asayansi, madokotala komanso akatswiri ena akufotokoza maganizo awo a mmene moyo unayambira atayerekezera zimene anapeza ndi zimene Baibulo limanena. TIMABUKU Mmene Moyo Unayambira—Mafunso 5 Ofunika Kwambiri Onani zimene umboni umanena kenako musankhe nokha kukhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa kapena zinakhalako zokha. TIMABUKU Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa? Zimene mumakhulupirira pa nkhani ya mmene moyo unayambira zimakhudza moyo wanu. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 4: Kodi Ndingafotokozere Bwanji Munthu Kuti Zinthu Zinachita Kulengedwa? Simukufunika kuchita kukhala wodziwa kwambiri sayansi kuti muthe kufotokozera munthu umboni wosonyeza kuti n’zomveka kukhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa. Gwiritsirani ntchito zitsanzo zosavuta kumva zopezeka m’Baibulo. KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Mulungu Anasintha Zamoyo Zina Polenga Mitundu Inanso ya Zamoyo? Baibulo silitsutsa zimene asayansi amanena zoti mitundu ya zamoyo imatulutsanso zamoyo zina zofanana ndi zamtundu womwewo. Mfundo Zofunika za M'Baibulo—Mavidiyo Kodi Zinthu Zakumwamba ndi Padziko Lapansi Zinachita Kulengedwa? Anthu ambiri samvetsa bwinobwino zimene Baibulo limanena zokhudza chilengedwe kapenanso amaganiza kuti ndi zongopeka. Kodi zimene Baibulo limanena zokhudza mmene chilengedwe chinayambira ndi zomveka?