Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Moyo Wanga Wachinyamata​—Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhulana Bwino ndi Makolo Anga?

Moyo Wanga Wachinyamata​—Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhulana Bwino ndi Makolo Anga?

Onani zimene Esther ndi Partik anachita kuti azilankhulana bwino ndi makolo awo komanso kuti azigwirizana nawo kwambiri.