Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zozizwitsa zimene Mulungu anachita poyankha pemphero la Hezekiya. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.