Mungaphunzire zambiri pa nkhani ya Yonatani ndi Davide. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.