Kodi mwatopa ndi anzanu amene amakulowetsani m’mavuto? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mmene mungapezere anzanu enieni komanso zimene mungachite kuti anthu azisangalala kucheza nanu.