Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ACHINYAMATA ACHITE

ZOTI MUCHITE

Zimene Mungachite Kuti Muthandize Ena

Njira zitatu zimene zingakuthandizeni pokonza mapulani oti muthandize ena

Zimene Mungachite Mukakhumudwa

Kodi n’chiyani chimene chingakuthandizeni kukhala wosangalala mukakhumudwa?

Kulimbana ndi Vuto la Mmene Mukumvera Mumtima

Zoti muchitezi zikuthandizani kuti mudziwe zimene mungachite mukamakumana ndi mavuto.

Kodi N’kungocheza Kapena Kukopana?

Nkhani imene munthu wina angaione ngati yocheza, wina angaione ngati yomukopa. Mungatani kuti muzipewa kutumiza mameseji olakwika?