Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ACHINYAMATA ACHITE

ZOTI MUCHITE

Mmene Mungafotokozere Zimene Mumakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana

Malangizo amene angakuthandizeni kufotokoza molimba mtima zimene mumakhulupirira.

Kodi Nthawi Zina Mumasowa Mpata Wochitira Zinthu Panokha?

Onani zimene mungachite kuti makolo anu azikudalirani.

Mmene Mungasankhire Munthu Womutsanzira

Gawoli likuthandizani kuti mudziwe amene mungamutsanzire.

Kodi Mungatani pa Nkhani ya Mowa?

Zoti muchitezi zikuthandizani kudziwa zoyenera kuchita ngati anzanu akukukakamizani kuti mumwe mowa.