Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ACHINYAMATA ACHITE

ZOTI MUCHITE

Muziganizira Kufunika kwa Zomwe Mumakhulupirira: Pa Nkhani ya Kudzisunga

Tsambali lingakuthandizeni kutsatira lamulo la Mulungu loletsa kugonana musanakhale pa banja.

Zimene Zingakuthandizeni Kuphunzira Chinenero China

Kuphunzira chinenero china kumafunika kuyeserera, nthawi ndi khama. Zoti muchitezi zikuthandizani kudziwa zoyenera kuchita pophunzira chinenero china.

Zimene Mungachite Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama

Gwiritsani ntchito zoti muchitezi kuti muone kuchuluka kwa zinthu zofunika ndi zongowonjezera komanso onani ngati zonse zikugwirizana ndi bajeti yanu.

Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu

Onani zimene zingakuthandizeni kukhala osamala musanatumize zithunzi.